1 Samueli 31:5 BL92

5 Ndipo pakuona kuti Sauli anafa, wonyamula zida zace yemwe, anagwera lupanga lace, nafera limodzi ndi iye.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 31

Onani 1 Samueli 31:5 nkhani