1 Samueli 31:4 BL92

4 Tsono Sauli ananena ndi wonyamula zida zace, Solola lupanga lako, undipyoze nalo; kuti osadulidwa awa angabwere ndi kundipyoza, ndi kundiseka, Koma woo nyamula zida zace anakana; cifukwa anaopa ndithu. Cifukwa cace Sauli anatenga lupanga lace naligwera.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 31

Onani 1 Samueli 31:4 nkhani