1 Samueli 31:3 BL92

3 Ndipo nkhondoyo inamkulira Sauli kwambiri, oponya mibvi nampeza; ndipo iye anasautsika kwakukuru cifukwa ca oponya mibviyo.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 31

Onani 1 Samueli 31:3 nkhani