9 Ndipo anadula mutu wace, natenga zida zace, natumiza m'dziko lonse la Afilisti mithenga yolalikira ku nyumba ya milungu yao, ndi kwa anthu.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 31
Onani 1 Samueli 31:9 nkhani