1 Samueli 31:8 BL92

8 Ndipo kunali m'mawa mwace, pakubwera Afilisti kubvula akufawo, anapeza Sauli ndi ana ace atatu ali akufa m'phiri la Giliboa.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 31

Onani 1 Samueli 31:8 nkhani