1 Samueli 4:21 BL92

21 Ndipo iye anamucha dzina la mwanayo Ikabodi, nati, Ulemerero wacoka kwa Israyeli; cifukwa likasa la Mulungu linalandidwa, ndi cifukwa ca mpongozi wace ndi mwamuna wace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 4

Onani 1 Samueli 4:21 nkhani