1 Samueli 5:3 BL92

3 Ndipo pakuuka a ku Asidodi mamawa, taonani Dagoni adagwa pansi, nagona cafufumimba patsogolo pa likasa la Yehova. Ndipo iwo anatenga Dagoni namuimikanso m'malo mwace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 5

Onani 1 Samueli 5:3 nkhani