1 Samueli 5:4 BL92

4 Ndipo m'mawa mwace polawirira, taonani, Dagoni adagwa pansi, nagona cafufumimba patsogolo pa likasa la Yehova; ndipo mutu wace ndi zikhato zonse ziwiri za manja ace zinagona zoduka paciundo; Dagoni anatsala thupi lokha.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 5

Onani 1 Samueli 5:4 nkhani