1 Samueli 6:17 BL92

17 Ndipo amenewa ndiwo mafundo agolidi amene anabwezera kwa Yehova akhale nsembe yoparamula, kwa Asidodi limodzi, kwa Gaza limodzi, kwa Asikeloni limodzi, kwa Gati limodzi, kwa Ekroni limodzi;

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 6

Onani 1 Samueli 6:17 nkhani