1 Samueli 6:18 BL92

18 ndiponso mbewa zagolidi, monga ciwerengo ca midzi yonse ya mafumu asanu a Afilisti, midzi ya malinga, ndi midzi ya kumiraga; kufikira ku mwala waukuru, adaikapo likasa la Yehova; mwalawo ulipobe kufikira lero m'munda wa Yoswa wa ku Betisemesi.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 6

Onani 1 Samueli 6:18 nkhani