1 Samueli 6:19 BL92

19 Ndipo Mulungu anakantha anthu a ku Betisemesi, cifukwa anasuzumira m'likasa la Yehova, anakantha anthu zikwi makumi asanu; ndipo anthu analira maliro, cifukwa Yehova anawakantha anthuwo ndi makanthidwe akuru.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 6

Onani 1 Samueli 6:19 nkhani