2 Ndipo Afilistiwo anaitana ansembe ndi oombeza, nati, Ticitenji ndi likasa la Yehova? mutidziwitse cimene tilitumize naco kumalo kwace.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 6
Onani 1 Samueli 6:2 nkhani