1 Samueli 6:3 BL92

3 Ndipo iwo anati, Ngati mulitumiza kwina likasa la Mulungu wa Israyeli, musalitumize lopanda kanthu; koma makamaka mulibweze ndi nsembe yoparamula, mukatero mudzaciritsidwa, ndi kudziwa cifukwa cace dzanja lace liri pa inu losacoka.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 6

Onani 1 Samueli 6:3 nkhani