1 Samueli 6:4 BL92

4 Ndipo iwo aja anati, Tidzambwezera nsembe yoparamula yanji? Ndipo iwo anati, Mafundo asanu agolidi, ndi mbewa zisanu zagolidi, monga mwa ciwerengo ca mafumu a Afilisti; popeza kusauka kumodzi kunali pa inu nonse, ndi pa mafumu anu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 6

Onani 1 Samueli 6:4 nkhani