1 Samueli 6:5 BL92

5 Cifukwa cace muzipanga zifanizo za mafundo anu, ndi zifanizo za mbewa zanu zimene ziipitsa dziko; ndipo mucitire ulemu Mulungu wa lsrayeli; kuti kapena adzaleza dzanja lace pa inu, ndi pa milungu yanu, ndi pa dziko lanu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 6

Onani 1 Samueli 6:5 nkhani