1 Samueli 6:6 BL92

6 Mulikuumitsiranji mitima yanu, monga Aaigupto ndi Farao anaumitsa mitima yao? Kodi iwo sana lola anthuwo amuke, iye atacita kodabwitsa pakati pao, ndipo anamuka?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 6

Onani 1 Samueli 6:6 nkhani