1 Samueli 7:11 BL92

11 Ndipo Aisrayeli anaturuka ku Mizipa, nathamangira Afilisti, nawakantha mpaka anafika pansi pa Betikara.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 7

Onani 1 Samueli 7:11 nkhani