12 Pamenepo Samueli anatenga mwala nauimika pakati pa Mizipa ndi Seni, naucha dzina lace. Ebenezeri, nati, Kufikira pano Yehovaanatithandiza.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 7
Onani 1 Samueli 7:12 nkhani