1 Samueli 7:13 BL92

13 Comweco anagonjetsa Afilisti, ndino iwo sanatumphanso malire a Israyeli ndipo dzanja la Yehova linasautsa Afilisti masiku onse a Samueli.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 7

Onani 1 Samueli 7:13 nkhani