1 Samueli 7:16 BL92

16 Ndipo anayenda cozungulira caka ndi caka ku Beteli, ndi ku Giligala, ndi ku Mizipa; naweruza Israyeli m'malo onse amenewa.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 7

Onani 1 Samueli 7:16 nkhani