17 Ndipo anabwera ku Rama, pakuti nyumba yace inali kumeneko; ndipo pamenepo anaweruza Israyeli; namangapo guwa la nsembe la Yehova.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 7
Onani 1 Samueli 7:17 nkhani