8 Ndipo ana a Israyeli anati kwa Samueli, Musaleke kutipempherera kwa Yehova Mulungu wathu, kuti iye atipulumutse m'manja a Afilistiwo.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 7
Onani 1 Samueli 7:8 nkhani