9 Ndipo Samueli anatenga mwana wa nkhosa woyamwa, nampereka wathunthu kwa Yehova, nsembe yopsereza; ndipo Samueli anapempherera Israyeli kwa Yehova; ndipo Yehova anambvomereza.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 7
Onani 1 Samueli 7:9 nkhani