20 kuti ifenso tikafanane nao anthu a mitundu yonse; kuti mfumu yathuyo ikatiweruzire, ndi kuturuka kutitsogolera, ndi kuponya nafe nkhondo zathu.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 8
Onani 1 Samueli 8:20 nkhani