5 nanena naye, Taonani, mwakalamba, ndipo ana anu satsanza makhalidwe anu; tsono, mutilongere mfumu kuti ikatiweruze, monga umo mucitidwa m'mitundu yonse ya anthu.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 8
Onani 1 Samueli 8:5 nkhani