1 Samueli 8:6 BL92

6 Koma cimeneci sicinakondweretsa Samueli, pamene iwo anati, Tipatseni mfumu kuti itiweruze. Ndipo Samueli anapemphera kwa Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 8

Onani 1 Samueli 8:6 nkhani