7 Ndipo Yehova ananena ndi Samueli, Umvere mau onse anthuwo alikulankhula nawe; popeza sindiwe anakukana, koma ndine anandikana, kuti ndisakhale mfumu yao.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 8
Onani 1 Samueli 8:7 nkhani