1 Samueli 8:8 BL92

8 Monga nchito zao zonse anazicita kuyambira tsiku lija ndinawaturutsa ku Aigupto, kufikira lero lino kuti anandisiya Ine, natumikira milungu yina, momwemo alikutero ndi iwenso.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 8

Onani 1 Samueli 8:8 nkhani