20 Za aburu ako atatayika adapita masiku atatu, usalingalirenso iwowa; pakuti anapezedwa. Ndipo cifuniro conse ca Israyeli ciri kwa yani? Si kwa iwe ndi banja lonse la atate wako?
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 9
Onani 1 Samueli 9:20 nkhani