1 Samueli 9:22 BL92

22 Ndipo Samueli anatenga Sauli ndi mnyamata wace, napita nao ku cipinda ca alendo, nawakhalitsa pa malo a ulemu pakati pa oitanidwa onse; ndiwo anthu monga makumi atatu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 9

Onani 1 Samueli 9:22 nkhani