1 Samueli 9:26 BL92

26 Ndipo anauka mamawa; ndipo kutaca, Samueli anaitana Sauli ali pamwamba pa nyumba, nati, Ukani kuti ndikuloleni mumuke. Ndipo Sauli anauka, naturuka onse awiri, iye ndi Samueli, kunka kunja.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 9

Onani 1 Samueli 9:26 nkhani