1 Samueli 9:27 BL92

27 Ndipo pamene analikutsika polekeza mudzi, Samueli ananena ndi Sauli, Uzani mnyamatayo abatsogola; napita iyeyo. Koma inu muime pano, kuti ndikumvetseni mau a Mulungu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 9

Onani 1 Samueli 9:27 nkhani