1 Pamenepo Samueli anatenga nsupa ya mafuta, nawatsanulira pamutu pace, nampsompsona iye, nati, Sanakudzozani ndi Mulungu kodi, mukhale mfumu ya pa colowa cace?
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 10
Onani 1 Samueli 10:1 nkhani