5 Pamene anafika ku dziko la Zufi, Sauli anamuuza mnyamata amene anali naye, kuti, Tiye tibwerere; kuti atate wanga angaleke kusamalira aburuwo, ndi kutenga nkhawa cifukwa ca ife.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 9
Onani 1 Samueli 9:5 nkhani