1 Samueli 9:8 BL92

8 Ndipo mnyamatayo anayankhanso kwa Sauli nati, Onani m'dzanja langa muli limodzi la magawo anai a sekeli wa siliva; ndidzampatsa munthu wa Mulungu limeneli kuti atiuze njira yathu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 9

Onani 1 Samueli 9:8 nkhani