Luka 14:27 BL92

27 Ndipo amene ali yense sasenza mtanda wace wa mwini yekha, ndi kudza pambuyo panga, sakhoza kukhala wophunzira wanga,

Werengani mutu wathunthu Luka 14

Onani Luka 14:27 nkhani