Luka 14:28 BL92

28 Pakuti ndani wa inu amene akafuna kumanga nsanja yaitali, sathanga wakhala pansi, nawerengera mtengo wace, aone ngati ali nazo zakuimariza?

Werengani mutu wathunthu Luka 14

Onani Luka 14:28 nkhani