Luka 8:46 BL92

46 Koma Yesu anati, Wina wandikhudza Ine; pakuti a ndazindikira Ine kuti mphamvu yaturuka mwa Ine.

Werengani mutu wathunthu Luka 8

Onani Luka 8:46 nkhani