Luka 9:27 BL92

27 Koma Ine ndinena ndi inu zoonadi, Kuli ena a iwo akuimirira pano, amene sadzalawatu imfa, kufikira kuti adzaona Ufumu wa Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Luka 9

Onani Luka 9:27 nkhani