1 Mbiri 10:12 BL92

12 anauka ngwazi zonse, nacotsa mtembo wa Sauli, ndi mitembo ya ana ace, nabwera nayo ku Yabesi, naika mafupa ao patsinde pa mtengo wathundu ku Yabesi, nasala masiku asanu ndi awiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 10

Onani 1 Mbiri 10:12 nkhani