1 Mbiri 10:13 BL92

13 Momwemo Sauli anafa, cifukwa ca kulakwa kwace analakwira Yehova, kulakwira mau a Yehova amene sanawasunga; ndiponso cifukwa ca kufunsira wobwebweta, kufunsirako,

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 10

Onani 1 Mbiri 10:13 nkhani