1 Mbiri 11:11 BL92

11 Kuwerenga kwa amphamvu aja Davide anali nao ndi uku: Yasobeamu mwana wa Mhakimoni, mkuru wa makumi atatu aja, anasamulira mazana atatu mkondo wace, nawapha nthawi imodzi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 11

Onani 1 Mbiri 11:11 nkhani