13 Anali pamodzi ndi Da vide ku Pasidamimu muja; Afilisti anasonkhanako kunkhondo kumene kunali munda wodzala ndi barele; ndipo anthu anathawa pamaso pa Afilisti.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 11
Onani 1 Mbiri 11:13 nkhani