1 Mbiri 11:14 BL92

14 Koma anadziimika pakati pa munda, naulanditsa, nakantha Afilisti; m'mwemo anawapulumutsa Yehova ndi cipulumutso cacikuru.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 11

Onani 1 Mbiri 11:14 nkhani