1 Mbiri 11:15 BL92

15 Ndipo atatu a akuru makumi atatu anatsikira kuthanthwe kwa Davide, ku phanga la Adulamu; ndi nkhondo ya Afilisti idamanga misasa m'cigwa ca Refaimu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 11

Onani 1 Mbiri 11:15 nkhani