1 Mbiri 11:17 BL92

17 Ndipo Davide analakalaka, nati, Ha! mwenzi wina atandimwetsa madzi a m'citsime ca ku Betelehemu ciri kucipata,

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 11

Onani 1 Mbiri 11:17 nkhani