1 Mbiri 11:18 BL92

18 Napyola atatuwo misasa ya Afilish natunga madzi ku citsime ca ku Betelehemu ciri kucipata, nabwera nao kwa Davide; koma Davide anakana kumwako, koma anawathirira kwa Yehova;

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 11

Onani 1 Mbiri 11:18 nkhani