1 Mbiri 11:20 BL92

20 Ndipo Abisai mbale wa Yoabu, ndiye wamkuru wa atatuwa; pakuti anasamulira mazana atatu mkondo wace, nawapha, namveka dzina pakati pa atatuwa.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 11

Onani 1 Mbiri 11:20 nkhani