1 Mbiri 12:15 BL92

15 Awa ndi omwe aja anaoloka Yordano mwezi woyamba, atadzala kusefukira magombe ace onse; nathawitsa onse okhala m'zigwa kum'mawa ndi kumadzulo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 12

Onani 1 Mbiri 12:15 nkhani