1 Mbiri 12:14 BL92

14 Awa a ana a Gadi, anali atsogoleri a nkhondo; wamng'ono wa iwo anayang'anira zana limodzi, ndi wamkuru wa iwo anayang'anira cikwi cimodzi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 12

Onani 1 Mbiri 12:14 nkhani